Ekisodo 32:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Choncho Mose anabwerera kwa Yehova ndi kunena kuti: “Aa, anthuwa achita tchimo lalikulu, chifukwa adzipangira mulungu wagolide!+ 1 Samueli 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tchimo la atumikiwa linakula kwambiri pamaso pa Yehova,+ chifukwa amuna amenewa sanali kulemekeza nsembe ya Yehova.+ 1 Mafumu 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye adzasiya Isiraeli+ chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita, ndiponso amene anachimwitsa nawo Isiraeli.”+
31 Choncho Mose anabwerera kwa Yehova ndi kunena kuti: “Aa, anthuwa achita tchimo lalikulu, chifukwa adzipangira mulungu wagolide!+
17 Tchimo la atumikiwa linakula kwambiri pamaso pa Yehova,+ chifukwa amuna amenewa sanali kulemekeza nsembe ya Yehova.+
16 Iye adzasiya Isiraeli+ chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita, ndiponso amene anachimwitsa nawo Isiraeli.”+