Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 12:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Chinthu chimenechi chinakhala chochimwitsa anthu.+ Anthuwo anali kukafika mpaka ku Dani kukaima pamaso pa chifaniziro cha mwana wa ng’ombecho.

  • 1 Mafumu 13:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Zimenezi zinachimwitsa nyumba yonse ya Yerobowamu,+ ndipo inayenera kuwonongedwa ndi kufafanizidwa padziko lapansi.+

  • 1 Mafumu 14:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma iweyo unayamba kuchita zinthu zoipa kwambiri kuposa onse amene anakhalapo iwe usanakhale. Unadzipangiranso mulungu wina+ ndi zifaniziro zopangidwa ndi zitsulo zosungunula+ kuti undikwiyitse,+ ndipo wandikankhira ineyo kumbuyo kwako.+

  • Mateyu 18:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Tsoka dzikoli chifukwa cha zopunthwitsa! Inde sitingachitire mwina, zopunthwitsazo ziyenera kubwera ndithu,+ koma tsoka lili kwa munthu wobweretsa chopunthwitsa!+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena