Nehemiya 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Koma iwo anakhala osamvera+ ndipo anakupandukirani.+ Anapitiriza kufulatira chilamulo chanu,+ ndipo anapha aneneri anu+ amene anali kuwalimbikitsa kuti abwerere kwa inu.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+ Salimo 50:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwe umadana ndi malangizo,*+Ndipo umaponya mawu anga kunkhongo.+ Ezekieli 23:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Popeza kuti wandiiwala+ ndi kundiponya kumbuyo,+ udzalangidwa chifukwa cha khalidwe lako lotayirira ndi zochita zako zauhule.’”
26 “Koma iwo anakhala osamvera+ ndipo anakupandukirani.+ Anapitiriza kufulatira chilamulo chanu,+ ndipo anapha aneneri anu+ amene anali kuwalimbikitsa kuti abwerere kwa inu.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+
35 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Popeza kuti wandiiwala+ ndi kundiponya kumbuyo,+ udzalangidwa chifukwa cha khalidwe lako lotayirira ndi zochita zako zauhule.’”