1 Mafumu 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma iweyo unayamba kuchita zinthu zoipa kwambiri kuposa onse amene anakhalapo iwe usanakhale. Unadzipangiranso mulungu wina+ ndi zifaniziro zopangidwa ndi zitsulo zosungunula+ kuti undikwiyitse,+ ndipo wandikankhira ineyo kumbuyo kwako.+ Nehemiya 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Koma iwo anakhala osamvera+ ndipo anakupandukirani.+ Anapitiriza kufulatira chilamulo chanu,+ ndipo anapha aneneri anu+ amene anali kuwalimbikitsa kuti abwerere kwa inu.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+
9 Koma iweyo unayamba kuchita zinthu zoipa kwambiri kuposa onse amene anakhalapo iwe usanakhale. Unadzipangiranso mulungu wina+ ndi zifaniziro zopangidwa ndi zitsulo zosungunula+ kuti undikwiyitse,+ ndipo wandikankhira ineyo kumbuyo kwako.+
26 “Koma iwo anakhala osamvera+ ndipo anakupandukirani.+ Anapitiriza kufulatira chilamulo chanu,+ ndipo anapha aneneri anu+ amene anali kuwalimbikitsa kuti abwerere kwa inu.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+