1 Mafumu 13:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Zimenezi zinachimwitsa nyumba yonse ya Yerobowamu,+ ndipo inayenera kuwonongedwa ndi kufafanizidwa padziko lapansi.+ 2 Mafumu 10:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma Yehu sanayesetse kuyenda motsatira malamulo a Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mtima wake wonse.+ Sanapatuke pa machimo a Yerobowamu amene anachimwitsa nawo Isiraeli.+ 2 Mafumu 17:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anang’amba Isiraeli kumuchotsa kunyumba ya Davide ndipo iwo analonga ufumu Yerobowamu mwana wa Nebati.+ Yerobowamuyo anasiyitsa Aisiraeli kutsatira Yehova n’kuwachimwitsa ndi tchimo lalikulu.+
34 Zimenezi zinachimwitsa nyumba yonse ya Yerobowamu,+ ndipo inayenera kuwonongedwa ndi kufafanizidwa padziko lapansi.+
31 Koma Yehu sanayesetse kuyenda motsatira malamulo a Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mtima wake wonse.+ Sanapatuke pa machimo a Yerobowamu amene anachimwitsa nawo Isiraeli.+
21 Anang’amba Isiraeli kumuchotsa kunyumba ya Davide ndipo iwo analonga ufumu Yerobowamu mwana wa Nebati.+ Yerobowamuyo anasiyitsa Aisiraeli kutsatira Yehova n’kuwachimwitsa ndi tchimo lalikulu.+