1 Mafumu 12:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chinthu chimenechi chinakhala chochimwitsa anthu.+ Anthuwo anali kukafika mpaka ku Dani kukaima pamaso pa chifaniziro cha mwana wa ng’ombecho. 1 Mafumu 13:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Zimenezi zinachimwitsa nyumba yonse ya Yerobowamu,+ ndipo inayenera kuwonongedwa ndi kufafanizidwa padziko lapansi.+ 1 Mafumu 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye adzasiya Isiraeli+ chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita, ndiponso amene anachimwitsa nawo Isiraeli.”+
30 Chinthu chimenechi chinakhala chochimwitsa anthu.+ Anthuwo anali kukafika mpaka ku Dani kukaima pamaso pa chifaniziro cha mwana wa ng’ombecho.
34 Zimenezi zinachimwitsa nyumba yonse ya Yerobowamu,+ ndipo inayenera kuwonongedwa ndi kufafanizidwa padziko lapansi.+
16 Iye adzasiya Isiraeli+ chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita, ndiponso amene anachimwitsa nawo Isiraeli.”+