Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 10:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Tsopano Aisiraeli inu, kodi Yehova Mulungu wanu akufuna kuti muzichita chiyani,+ koposa kuopa+ Yehova Mulungu wanu kuti muziyenda m’njira zake zonse,+ kukonda+ ndi kutumikira Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse,+

  • 1 Mafumu 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Komanso kuti Yehova adzakwaniritse mawu ake okhudza ine amene analankhula,+ akuti, ‘Ana ako+ akadzasamalira njira zawo, mwa kuyenda+ mokhulupirika*+ pamaso panga ndi mtima wawo wonse+ ndi moyo wawo wonse, munthu wa m’banja lako sadzachoka pampando wachifumu wa Isiraeli.’+

  • Salimo 78:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Iwo sanasunge pangano la Mulungu,+

      Ndipo anakana kutsatira chilamulo chake.+

  • Miyambo 4:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Uteteze mtima wako kuposa zonse zimene ziyenera kutetezedwa,+ pakuti mumtimamo ndiye muli akasupe a moyo.+

  • Hoseya 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno Yehova anauza Hoseya kuti: “Mwanayu umupatse dzina lakuti Yezereeli,+ pakuti kwatsala kanthawi kochepa kuti ndiimbe Yezereeli* mlandu wokhetsa magazi, mlandu wa nyumba ya Yehu.+ Pamenepo ndidzathetsa ufumu wolamulira nyumba ya Isiraeli,+

  • Aheberi 10:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 “Koma wolungama wanga adzakhala ndi moyo mwa chikhulupiriro chake,”+ ndipo “ngati wabwerera m’mbuyo, ine sindikondwera naye.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena