Habakuku 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Taona! Iye wadzitukumula+ ndipo si wowongoka mtima. Koma wolungama adzakhalabe ndi moyo mwa chikhulupiriro chake.+ 1 Yohane 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amenewo anachoka pakati pathu, koma sanali m’gulu lathu,+ chifukwa akanakhala a m’gulu lathu, akanakhalabe ndi ife.+ Sikuti onse ali m’gulu lathu ayi, ndipo iwo achoka m’gulu lathu, kuti zimenezi zidziwike.+
4 “Taona! Iye wadzitukumula+ ndipo si wowongoka mtima. Koma wolungama adzakhalabe ndi moyo mwa chikhulupiriro chake.+
19 Amenewo anachoka pakati pathu, koma sanali m’gulu lathu,+ chifukwa akanakhala a m’gulu lathu, akanakhalabe ndi ife.+ Sikuti onse ali m’gulu lathu ayi, ndipo iwo achoka m’gulu lathu, kuti zimenezi zidziwike.+