Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 17:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma iwo sanamvere. M’malomwake anaumitsa makosi awo,+ ngati mmene makolo awo anaumitsira makosi awo. Makolo awowo sanasonyeze chikhulupiriro+ mwa Yehova Mulungu wawo.

  • 2 Mbiri 13:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kodi simunathamangitse ansembe a Yehova,+ omwe ndi ana a Aroni, komanso Alevi? Ndipo kodi simukudziikira ansembe ngati mmene amachitira anthu a mayiko ena?+ Aliyense amene wabwera n’kudziika pa udindo waunsembe mwa kupereka ng’ombe yaing’ono yamphongo ndi nkhosa zamphongo 7, amakhala wansembe wa mafano omwe si milungu.+

  • Nehemiya 9:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “Koma iwo anakhala osamvera+ ndipo anakupandukirani.+ Anapitiriza kufulatira chilamulo chanu,+ ndipo anapha aneneri anu+ amene anali kuwalimbikitsa kuti abwerere kwa inu.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena