2 Mbiri 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Aleviwo anasiya malo awo odyetserako ziweto+ ndi madera awo+ n’kupita ku Yuda ndi ku Yerusalemu,+ chifukwa Yerobowamu+ ndi ana ake anachotsa+ Aleviwo pa udindo wokhala ansembe a Yehova.
14 Aleviwo anasiya malo awo odyetserako ziweto+ ndi madera awo+ n’kupita ku Yuda ndi ku Yerusalemu,+ chifukwa Yerobowamu+ ndi ana ake anachotsa+ Aleviwo pa udindo wokhala ansembe a Yehova.