Ekisodo 32:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno Mose anakaima pachipata cha msasawo, ndipo anati: “Ndani ali kumbali ya Yehova? Abwere kwa ine!”+ Ndipo ana onse aamuna a Levi anayamba kusonkhana kwa Mose. Deuteronomo 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo kwa Levi anati:+“Tumimu ndi Urimu+ wanu ndizo za munthu wokhulupirika kwa inu,+Amene munamuyesa pa Masa.+Munayamba kulimbana naye pafupi ndi madzi a Meriba.+
26 Ndiyeno Mose anakaima pachipata cha msasawo, ndipo anati: “Ndani ali kumbali ya Yehova? Abwere kwa ine!”+ Ndipo ana onse aamuna a Levi anayamba kusonkhana kwa Mose.
8 Ndipo kwa Levi anati:+“Tumimu ndi Urimu+ wanu ndizo za munthu wokhulupirika kwa inu,+Amene munamuyesa pa Masa.+Munayamba kulimbana naye pafupi ndi madzi a Meriba.+