2 Samueli 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhazikika pamaso pako mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+ 1 Mbiri 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘“Masiku ako akadzakwana kuti ukakhale pamodzi ndi makolo ako,+ pamenepo ndithu ndidzautsa mbewu yako yobwera pambuyo pako,+ imene idzakhala mmodzi wa ana ako, ndipo ndidzakhazikitsadi ufumu wake.+ 1 Mbiri 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Taona, udzabala mwana.+ Mwana ameneyo adzakhala munthu wabata, ndipo ndidzam’patsa mpumulo pakati pa adani ake onse omuzungulira.+ N’chifukwa chake dzina lake adzakhala Solomo,*+ ndipo m’masiku ake ndidzakhazikitsa mtendere+ ndi bata pa Isiraeli. 1 Mbiri 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Akamatsatira malamulo anga+ ndi zigamulo zanga+ ndi mtima wonse ngati mmene akuchitira lero, ine ndidzakhazikitsa ufumu wake+ ndipo sudzagwedezeka mpaka kalekale.’ Salimo 89:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndalumbira kamodzi kokha pa kuyera kwanga,+Davide sindidzamunamiza.+ Salimo 132:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova walumbira kwa Davide,+Ndithudi sadzabweza mawu ake akuti:+“Ndidzaika pampando wako wachifumu+Chipatso cha mimba yako.+
16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhazikika pamaso pako mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+
11 “‘“Masiku ako akadzakwana kuti ukakhale pamodzi ndi makolo ako,+ pamenepo ndithu ndidzautsa mbewu yako yobwera pambuyo pako,+ imene idzakhala mmodzi wa ana ako, ndipo ndidzakhazikitsadi ufumu wake.+
9 Taona, udzabala mwana.+ Mwana ameneyo adzakhala munthu wabata, ndipo ndidzam’patsa mpumulo pakati pa adani ake onse omuzungulira.+ N’chifukwa chake dzina lake adzakhala Solomo,*+ ndipo m’masiku ake ndidzakhazikitsa mtendere+ ndi bata pa Isiraeli.
7 Akamatsatira malamulo anga+ ndi zigamulo zanga+ ndi mtima wonse ngati mmene akuchitira lero, ine ndidzakhazikitsa ufumu wake+ ndipo sudzagwedezeka mpaka kalekale.’
11 Yehova walumbira kwa Davide,+Ndithudi sadzabweza mawu ake akuti:+“Ndidzaika pampando wako wachifumu+Chipatso cha mimba yako.+