1 Mbiri 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzamukhazikitsa iye kukhala woyang’anira nyumba yanga+ ndi ufumu wanga+ mpaka kalekale, ndipo mpando wake wachifumu+ sudzatha mpaka kalekale.”’” Salimo 72:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo adzakhala ndi anthu omugonjera kuchokera kunyanja kukafika kunyanja,+Komanso kuchokera ku Mtsinje*+ kukafika kumalekezero a dziko lapansi.+
14 Ndidzamukhazikitsa iye kukhala woyang’anira nyumba yanga+ ndi ufumu wanga+ mpaka kalekale, ndipo mpando wake wachifumu+ sudzatha mpaka kalekale.”’”
8 Ndipo adzakhala ndi anthu omugonjera kuchokera kunyanja kukafika kunyanja,+Komanso kuchokera ku Mtsinje*+ kukafika kumalekezero a dziko lapansi.+