Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 89:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Mbewu yake idzakhala mpaka kalekale,+

      Ndipo mpando wake wachifumu udzakhala ngati dzuwa pamaso panga.+

  • Yeremiya 33:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 ndiye kuti inenso ndingathe kuphwanya pangano langa ndi Davide mtumiki wanga+ kuti asakhale ndi mwana woti adzalamulire monga mfumu pampando wachifumu wa Davide.+ Ndingachitenso chimodzimodzi ndi atumiki anga, ansembe achilevi.+

  • Luka 1:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Ameneyu adzakhala wamkulu+ ndipo adzatchedwa Mwana wa Wam’mwambamwamba.+ Yehova Mulungu adzam’patsa mpando wachifumu+ wa Davide atate wake.+

  • Aheberi 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma ponena za Mwana wake, iye akuti: “Mulungu ndiye mpando wako wachifumu mpaka muyaya,+ ndipo ndodo ya ufumu+ wako ndiyo ndodo yachilungamo.+

  • Chivumbulutso 3:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Wopambana pa nkhondo+ ndidzamulola kukhala nane pampando wanga wachifumu,+ monga mmene ine ndinakhalira+ ndi Atate wanga pampando wawo wachifumu+ nditapambana pa nkhondo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena