Genesis 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+ Numeri 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzamuona,+ koma si nthawi ino;Ndidzam’penya, koma si panopo.Ndithu nyenyezi+ idzatuluka mwa Yakobo,Ndodo yachifumu idzatulukadi mu Isiraeli.+Ndipo iye adzaphwanya chipumi cha Mowabu+Ndi chigaza cha ana onse ankhondo. Salimo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mitunduyo udzaiswa ndi ndodo yachifumu yachitsulo,+Udzaiphwanya ngati mbiya yadothi, n’kukhala zidutswazidutswa.”+
10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+
17 Ndidzamuona,+ koma si nthawi ino;Ndidzam’penya, koma si panopo.Ndithu nyenyezi+ idzatuluka mwa Yakobo,Ndodo yachifumu idzatulukadi mu Isiraeli.+Ndipo iye adzaphwanya chipumi cha Mowabu+Ndi chigaza cha ana onse ankhondo.
9 Mitunduyo udzaiswa ndi ndodo yachifumu yachitsulo,+Udzaiphwanya ngati mbiya yadothi, n’kukhala zidutswazidutswa.”+