Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 49:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+

  • Salimo 45:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Mulungu ndiye mpando wako wachifumu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+

      Ndodo yako yachifumu ndiyo ndodo yachilungamo.+

  • Salimo 108:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Giliyadi+ ndi wanga ndipo Manase+ ndi wanganso.

      Efuraimu ndi malo otetezeka a mtsogoleri amene ine ndamuika.+

      Yuda ndi ndodo yanga ya mtsogoleri wa asilikali.+

  • Salimo 110:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Yehova adzatambasula ndodo+ yako yachifumu yamphamvu kuchokera m’Ziyoni+ ndi kunena kuti:

      “Pita ukagonjetse anthu pakati pa adani ako.”+

  • Aheberi 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma ponena za Mwana wake, iye akuti: “Mulungu ndiye mpando wako wachifumu mpaka muyaya,+ ndipo ndodo ya ufumu+ wako ndiyo ndodo yachilungamo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena