Yoswa 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anapatsidwanso dera la Giliyadi, la Agesuri,+ la Amaakati, phiri lonse la Herimoni,+ ndi dera lonse la Basana+ mpaka ku Saleka.+ 2 Samueli 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kumeneko anamulonga ufumu kuti azilamulira Giliyadi,+ Aasere, Yezereeli,+ Efuraimu+ ndi Benjamini,+ Isiraeli yense.
11 Anapatsidwanso dera la Giliyadi, la Agesuri,+ la Amaakati, phiri lonse la Herimoni,+ ndi dera lonse la Basana+ mpaka ku Saleka.+
9 Kumeneko anamulonga ufumu kuti azilamulira Giliyadi,+ Aasere, Yezereeli,+ Efuraimu+ ndi Benjamini,+ Isiraeli yense.