Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 8:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Davide anagonjetsanso Amowabu+ ndi kuwayeza ndi chingwe. Iye anawagoneka pansi kuti ayeze zingwe ziwiri ndi kuwapha, ndiponso chingwe chimodzi chathunthu n’kuwasiya amoyo.+ Choncho Amowabu anakhala atumiki a Davide+ ndipo anali kukhoma msonkho kwa iye.+

  • 1 Mbiri 18:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kenako anagonjetsa Mowabu,+ moti Amowabuwo anakhala atumiki a Davide ndipo anali kukhoma msonkho kwa iye.+

  • Salimo 108:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Mowabu+ ndi beseni langa losambiramo.+

      Ndidzaponyera Edomu+ nsapato zanga.+

      Ndidzafuula mosangalala+ chifukwa chogonjetsa Filisitiya.”+

  • Salimo 110:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Adzapereka chiweruzo pakati pa anthu a mitundu ina.+

      Adzachititsa mitembo ya anthu kupezeka paliponse.+

      Adzaphwanyaphwanya mtsogoleri wa dziko la anthu ambiri.+

  • Yeremiya 48:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 ‘Anthu othawa aima chilili mumthunzi wa Hesiboni ndipo alibe mphamvu. Moto udzachokera ku Hesiboni+ ndipo malawi a moto adzachokera ku Sihoni+ ndi kutentha Mowabu m’mutu, m’mphepete mwa makutu, komanso paliwombo pa ana osokoneza.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena