Deuteronomo 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa chake n’chakuti, sanakuthandizeni+ ndi mkate ndi madzi pamene munali pa ulendo mutatuluka mu Iguputo,+ ndiponso chifukwa chakuti analemba ganyu Balamu mwana wa Beori, amene kwawo ndi ku Petori ku Mesopotamiya kuti akutemberereni.+ Deuteronomo 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Musachite kanthu kowathandiza kupeza mtendere ndi chitukuko masiku onse a moyo wanu, mpaka kalekale.+
4 Chifukwa chake n’chakuti, sanakuthandizeni+ ndi mkate ndi madzi pamene munali pa ulendo mutatuluka mu Iguputo,+ ndiponso chifukwa chakuti analemba ganyu Balamu mwana wa Beori, amene kwawo ndi ku Petori ku Mesopotamiya kuti akutemberereni.+
6 Musachite kanthu kowathandiza kupeza mtendere ndi chitukuko masiku onse a moyo wanu, mpaka kalekale.+