Ekisodo 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anthu adzamva+ ndipo adzatekeseka.+Okhala ku Filisitiya adzamva zopweteka ngati za pobereka.+ 2 Samueli 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Afilisiti+ anabwera kudzachita nkhondo ndi Isiraeli. Pamenepo Davide ndi atumiki ake anapita komweko n’kumenyana ndi Afilisiti, ndipo Davide anatopa.
15 Ndiyeno Afilisiti+ anabwera kudzachita nkhondo ndi Isiraeli. Pamenepo Davide ndi atumiki ake anapita komweko n’kumenyana ndi Afilisiti, ndipo Davide anatopa.