Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 24:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndidzamuona,+ koma si nthawi ino;

      Ndidzam’penya, koma si panopo.

      Ndithu nyenyezi+ idzatuluka mwa Yakobo,

      Ndodo yachifumu idzatulukadi mu Isiraeli.+

      Ndipo iye adzaphwanya chipumi cha Mowabu+

      Ndi chigaza cha ana onse ankhondo.

  • Oweruza 3:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Pa nthawi imeneyo anakantha amuna achimowabu 10,000.+ Aliyense mwa amunawo anali wojintcha+ ndipo aliyense wa iwo anali mwamuna wolimba mtima, koma palibe ngakhale mmodzi amene anapulumuka.+

  • 1 Samueli 14:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Tsopano Sauli analimbitsa ufumu wake mu Isiraeli+ ndipo anamenya nkhondo ndi adani ake onse om’zungulira. Iye anamenyana ndi Mowabu,+ ana a Amoni,+ Edomu,+ mafumu a Zoba+ ndi Afilisiti.+ Kulikonse kumene anali kutembenukira anali kuwalanga.+

  • Salimo 60:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Mowabu ndi beseni langa losambiramo.+

      Ndidzaponyera Edomu nsapato zanga.+

      Ndidzafuula mosangalala chifukwa chogonjetsa Filisitiya.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena