Salimo 60:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mowabu ndi beseni langa losambiramo.+ Edomu ndidzamuponyera nsapato zanga.+ Ndidzafuula mosangalala chifukwa chogonjetsa Filisitiya.”+
8 Mowabu ndi beseni langa losambiramo.+ Edomu ndidzamuponyera nsapato zanga.+ Ndidzafuula mosangalala chifukwa chogonjetsa Filisitiya.”+