Numeri 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzamuona, koma osati panopa;Ndidzamupenya, koma osati posachedwa. Nyenyezi+ idzatuluka mwa Yakobo,Ndodo yachifumu+ idzatuluka mu Isiraeli.+ Ndipo iye adzaphwanyadi chipumi cha Mowabu+Ndi mitu ya asilikali onse ankhanza. 2 Samueli 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Davide anagonjetsanso Amowabu+ ndipo anawagoneka pansi nʼkuyamba kuwayeza ndi chingwe. Ankati akayeza zingwe ziwiri, anthu amenewo ankawapha ndipo akayeza chingwe chimodzi, amenewo ankawasiya ndi moyo.+ Amowabuwo anakhala atumiki a Davide ndipo ankapereka msonkho kwa iye.+
17 Ndidzamuona, koma osati panopa;Ndidzamupenya, koma osati posachedwa. Nyenyezi+ idzatuluka mwa Yakobo,Ndodo yachifumu+ idzatuluka mu Isiraeli.+ Ndipo iye adzaphwanyadi chipumi cha Mowabu+Ndi mitu ya asilikali onse ankhanza.
2 Davide anagonjetsanso Amowabu+ ndipo anawagoneka pansi nʼkuyamba kuwayeza ndi chingwe. Ankati akayeza zingwe ziwiri, anthu amenewo ankawapha ndipo akayeza chingwe chimodzi, amenewo ankawasiya ndi moyo.+ Amowabuwo anakhala atumiki a Davide ndipo ankapereka msonkho kwa iye.+