Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 24:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndidzamuona, koma osati panopa;

      Ndidzamupenya, koma osati posachedwa.

      Nyenyezi+ idzatuluka mwa Yakobo,

      Ndodo yachifumu+ idzatuluka mu Isiraeli.+

      Ndipo iye adzaphwanyadi chipumi cha Mowabu+

      Ndi mitu ya asilikali onse ankhanza.

  • Oweruza 3:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Pa nthawi imeneyo anapha Amowabu pafupifupi 10,000.+ Onse anali asilikali amphamvu komanso olimba mtima, koma panalibe ngakhale mmodzi amene anapulumuka.+

  • 1 Samueli 14:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Sauli analimbitsa ufumu wake mu Isiraeli ndipo anamenyana ndi adani ake mʼmadera onse. Anamenyana ndi Amowabu,+ Aamoni,+ Aedomu,+ mafumu a Zoba+ ndi Afilisiti.+ Kulikonse kumene ankapita ankagonjetsa adani akewo.

  • Salimo 60:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Mowabu ndi beseni langa losambiramo.+

      Edomu ndidzamuponyera nsapato zanga.+

      Ndidzafuula mosangalala chifukwa chogonjetsa Filisitiya.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena