Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 24:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndidzamuona,+ koma si nthawi ino;

      Ndidzam’penya, koma si panopo.

      Ndithu nyenyezi+ idzatuluka mwa Yakobo,

      Ndodo yachifumu idzatulukadi mu Isiraeli.+

      Ndipo iye adzaphwanya chipumi cha Mowabu+

      Ndi chigaza cha ana onse ankhondo.

  • 2 Samueli 8:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Davide anagonjetsanso Amowabu+ ndi kuwayeza ndi chingwe. Iye anawagoneka pansi kuti ayeze zingwe ziwiri ndi kuwapha, ndiponso chingwe chimodzi chathunthu n’kuwasiya amoyo.+ Choncho Amowabu anakhala atumiki a Davide+ ndipo anali kukhoma msonkho kwa iye.+

  • Salimo 108:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Mowabu+ ndi beseni langa losambiramo.+

      Ndidzaponyera Edomu+ nsapato zanga.+

      Ndidzafuula mosangalala+ chifukwa chogonjetsa Filisitiya.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena