2 Mafumu 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mesa+ mfumu ya Mowabu anali woweta nkhosa. Ankapereka kwa mfumu ya Isiraeli ana a nkhosa 100,000, ndi nkhosa zamphongo zosameta ubweya zokwana 100,000 monga msonkho. 2 Mbiri 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Aamoni+ anayamba kupereka msonkho+ kwa Uziya. Pomalizira pake, kutchuka kwake+ kunafika mpaka ku Iguputo chifukwa anasonyeza mphamvu zochuluka zedi. Salimo 72:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mafumu a ku Tarisi ndi m’zilumba+Adzapereka msonkho.+Mafumu a ku Sheba ndi SebaAdzapereka mphatso.+
4 Mesa+ mfumu ya Mowabu anali woweta nkhosa. Ankapereka kwa mfumu ya Isiraeli ana a nkhosa 100,000, ndi nkhosa zamphongo zosameta ubweya zokwana 100,000 monga msonkho.
8 Ndiyeno Aamoni+ anayamba kupereka msonkho+ kwa Uziya. Pomalizira pake, kutchuka kwake+ kunafika mpaka ku Iguputo chifukwa anasonyeza mphamvu zochuluka zedi.
10 Mafumu a ku Tarisi ndi m’zilumba+Adzapereka msonkho.+Mafumu a ku Sheba ndi SebaAdzapereka mphatso.+