Genesis 19:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Nayenso mwana wamng’onoyo anabereka mwana wamwamuna, n’kumutcha dzina lakuti Beni-ami. Iye ndiye tate wa ana a Amoni+ mpaka lero. Oweruza 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ndipo anaiuza kuti: “Yefita wanena kuti, ‘Aisiraeli sanatenge dziko la Mowabu+ ndi dziko la ana a Amoni.+
38 Nayenso mwana wamng’onoyo anabereka mwana wamwamuna, n’kumutcha dzina lakuti Beni-ami. Iye ndiye tate wa ana a Amoni+ mpaka lero.
15 ndipo anaiuza kuti: “Yefita wanena kuti, ‘Aisiraeli sanatenge dziko la Mowabu+ ndi dziko la ana a Amoni.+