2 Samueli 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Davide anagonjetsanso Amowabu+ ndi kuwayeza ndi chingwe. Iye anawagoneka pansi kuti ayeze zingwe ziwiri ndi kuwapha, ndiponso chingwe chimodzi chathunthu n’kuwasiya amoyo.+ Choncho Amowabu anakhala atumiki a Davide+ ndipo anali kukhoma msonkho kwa iye.+ 2 Mafumu 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mesa+ mfumu ya Mowabu anali woweta nkhosa. Ankapereka kwa mfumu ya Isiraeli ana a nkhosa 100,000, ndi nkhosa zamphongo zosameta ubweya zokwana 100,000 monga msonkho.
2 Davide anagonjetsanso Amowabu+ ndi kuwayeza ndi chingwe. Iye anawagoneka pansi kuti ayeze zingwe ziwiri ndi kuwapha, ndiponso chingwe chimodzi chathunthu n’kuwasiya amoyo.+ Choncho Amowabu anakhala atumiki a Davide+ ndipo anali kukhoma msonkho kwa iye.+
4 Mesa+ mfumu ya Mowabu anali woweta nkhosa. Ankapereka kwa mfumu ya Isiraeli ana a nkhosa 100,000, ndi nkhosa zamphongo zosameta ubweya zokwana 100,000 monga msonkho.