Salimo 79:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsanulirani mkwiyo wanu pa mitundu ya anthu amene akukunyalanyazani,+Ndi pa maufumu amene sakuitana pa dzina lanu.+ Salimo 149:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kuti abwezere anthu a mitundu ina,+Ndi kudzudzula mitundu ya anthu,+
6 Tsanulirani mkwiyo wanu pa mitundu ya anthu amene akukunyalanyazani,+Ndi pa maufumu amene sakuitana pa dzina lanu.+