Numeri 31:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uwabwezere+ Amidiyani+ pa zimene anachitira ana a Isiraeli. Pambuyo pake udzaikidwa m’manda kuti ukagone ndi makolo ako.”+ Salimo 79:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsanulirani mkwiyo wanu pa mitundu ya anthu amene akukunyalanyazani,+Ndi pa maufumu amene sakuitana pa dzina lanu.+ Salimo 110:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Adzapereka chiweruzo pakati pa anthu a mitundu ina.+Adzachititsa mitembo ya anthu kupezeka paliponse.+Adzaphwanyaphwanya mtsogoleri wa dziko la anthu ambiri.+
2 “Uwabwezere+ Amidiyani+ pa zimene anachitira ana a Isiraeli. Pambuyo pake udzaikidwa m’manda kuti ukagone ndi makolo ako.”+
6 Tsanulirani mkwiyo wanu pa mitundu ya anthu amene akukunyalanyazani,+Ndi pa maufumu amene sakuitana pa dzina lanu.+
6 Adzapereka chiweruzo pakati pa anthu a mitundu ina.+Adzachititsa mitembo ya anthu kupezeka paliponse.+Adzaphwanyaphwanya mtsogoleri wa dziko la anthu ambiri.+