Numeri 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pambuyo poliona dzikolo, udzaikidwa m’manda kuti ukagone ndi makolo ako.+ Ndithudi, iweyo udzaikidwa m’manda mofanana ndi Aroni m’bale wako,+ Deuteronomo 32:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Pamenepo ukafera m’phiri limene ukukwera ndi kugona ndi makolo ako,+ monga mmene Aroni m’bale wako anafera m’phiri la Hora+ ndi kugona ndi makolo ake.
13 Pambuyo poliona dzikolo, udzaikidwa m’manda kuti ukagone ndi makolo ako.+ Ndithudi, iweyo udzaikidwa m’manda mofanana ndi Aroni m’bale wako,+
50 Pamenepo ukafera m’phiri limene ukukwera ndi kugona ndi makolo ako,+ monga mmene Aroni m’bale wako anafera m’phiri la Hora+ ndi kugona ndi makolo ake.