Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 7:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhazikika pamaso pako mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+

  • 2 Samueli 23:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Kodi si mmene nyumba yanga ilili kwa Mulungu?+

      Chifukwa chakuti anachita nane pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale,+

      Analikonza bwino ndipo n’lotetezeka.+

      Chifukwa ndilo chipulumutso changa+ ndi chondikondweretsa,

      Kodi chimenechi sindicho chifukwa chake adzakulitsa panganoli?+

  • Salimo 89:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Sindidzaphwanya pangano langa,+

      Ndipo sindidzasintha mawu otuluka pakamwa panga.+

  • Salimo 132:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yehova walumbira kwa Davide,+

      Ndithudi sadzabweza mawu ake akuti:+

      “Ndidzaika pampando wako wachifumu+

      Chipatso cha mimba yako.+

  • Yesaya 55:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tcherani khutu+ lanu ndipo bwerani kwa ine.+ Mvetserani ndipo mudzakhalabe ndi moyo.+ Ine ndidzachita nanu pangano lokhalapo mpaka kalekale+ lokhudza kukoma mtima kwanga kosatha kosonyezedwa kwa Davide, kumene kuli kokhulupirika.+

  • Yeremiya 31:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Yehova wanena kuti: “‘Ngati kumwamba kungayezedwe ndipo ngati maziko a dziko lapansi angafufuzidwe,+ inenso ndingakane anthu onse amene ndi mbewu ya Isiraeli chifukwa cha zonse zimene achita,’+ watero Yehova.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena