2 Samueli 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhazikika pamaso pako mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+ 1 Mafumu 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 inenso ndidzakhazikitsa mpando wako wachifumu mu ufumu wa Isiraeli mpaka kalekale, monga momwe ndinalonjezera Davide bambo ako kuti, ‘Munthu wa m’banja lako sadzachoka pampando wachifumu wa Isiraeli.’+ 1 Mbiri 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘“Masiku ako akadzakwana kuti ukakhale pamodzi ndi makolo ako,+ pamenepo ndithu ndidzautsa mbewu yako yobwera pambuyo pako,+ imene idzakhala mmodzi wa ana ako, ndipo ndidzakhazikitsadi ufumu wake.+ Salimo 89:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu anati: “Ndachita pangano ndi wosankhidwa wanga.+Ndalumbira kwa Davide mtumiki wanga,+ Salimo 89:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndidzamusonyeza kukoma mtima kwanga kosatha mpaka kalekale,+Ndipo pangano limene ndinachita naye silidzaphwanyidwa.+ Salimo 132:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova walumbira kwa Davide,+Ndithudi sadzabweza mawu ake akuti:+“Ndidzaika pampando wako wachifumu+Chipatso cha mimba yako.+
16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhazikika pamaso pako mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+
5 inenso ndidzakhazikitsa mpando wako wachifumu mu ufumu wa Isiraeli mpaka kalekale, monga momwe ndinalonjezera Davide bambo ako kuti, ‘Munthu wa m’banja lako sadzachoka pampando wachifumu wa Isiraeli.’+
11 “‘“Masiku ako akadzakwana kuti ukakhale pamodzi ndi makolo ako,+ pamenepo ndithu ndidzautsa mbewu yako yobwera pambuyo pako,+ imene idzakhala mmodzi wa ana ako, ndipo ndidzakhazikitsadi ufumu wake.+
3 Mulungu anati: “Ndachita pangano ndi wosankhidwa wanga.+Ndalumbira kwa Davide mtumiki wanga,+ Salimo 89:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndidzamusonyeza kukoma mtima kwanga kosatha mpaka kalekale,+Ndipo pangano limene ndinachita naye silidzaphwanyidwa.+ Salimo 132:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova walumbira kwa Davide,+Ndithudi sadzabweza mawu ake akuti:+“Ndidzaika pampando wako wachifumu+Chipatso cha mimba yako.+
28 Ndidzamusonyeza kukoma mtima kwanga kosatha mpaka kalekale,+Ndipo pangano limene ndinachita naye silidzaphwanyidwa.+
11 Yehova walumbira kwa Davide,+Ndithudi sadzabweza mawu ake akuti:+“Ndidzaika pampando wako wachifumu+Chipatso cha mimba yako.+