Mateyu 27:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Koma kapitawo wa asilikali ndi ena amene anali naye polondera Yesu ataona chivomezicho ndi zimene zimachitikazo, anachita mantha kwambiri ndipo anati: “Ndithudi, uyu analidi Mwana wa Mulungu.”+ Yohane 1:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Natanayeli anamuyankha kuti: “Rabi, ndinudi Mwana wa Mulungu,+ ndinu Mfumu+ ya Isiraeli.”
54 Koma kapitawo wa asilikali ndi ena amene anali naye polondera Yesu ataona chivomezicho ndi zimene zimachitikazo, anachita mantha kwambiri ndipo anati: “Ndithudi, uyu analidi Mwana wa Mulungu.”+