Maliko 15:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Tsopano, kapitawo wa asilikali amene anaimirira chapafupi moyang’ana Yesu, ataona zimene zinachitika pa nthawi imene anatsirizika, ananena kuti: “Ndithudi munthu uyu analidi Mwana wa Mulungu.”+ Luka 23:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Poona zochitikazo, kapitawo wa asilikali anayamba kutamanda Mulungu kuti: “Ndithudi munthu uyu anali wolungama.”+
39 Tsopano, kapitawo wa asilikali amene anaimirira chapafupi moyang’ana Yesu, ataona zimene zinachitika pa nthawi imene anatsirizika, ananena kuti: “Ndithudi munthu uyu analidi Mwana wa Mulungu.”+
47 Poona zochitikazo, kapitawo wa asilikali anayamba kutamanda Mulungu kuti: “Ndithudi munthu uyu anali wolungama.”+