Mateyu 27:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Koma kapitawo wa asilikali ndi ena amene anali naye polondera Yesu ataona chivomezicho ndi zimene zimachitikazo, anachita mantha kwambiri ndipo anati: “Ndithudi, uyu analidi Mwana wa Mulungu.”+ Luka 23:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Poona zochitikazo, kapitawo wa asilikali anayamba kutamanda Mulungu kuti: “Ndithudi munthu uyu anali wolungama.”+
54 Koma kapitawo wa asilikali ndi ena amene anali naye polondera Yesu ataona chivomezicho ndi zimene zimachitikazo, anachita mantha kwambiri ndipo anati: “Ndithudi, uyu analidi Mwana wa Mulungu.”+
47 Poona zochitikazo, kapitawo wa asilikali anayamba kutamanda Mulungu kuti: “Ndithudi munthu uyu anali wolungama.”+