Deuteronomo 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Ansembe, ana a Levi, azifika pafupi chifukwa ndi amene Yehova Mulungu wanu wawasankha kuti am’tumikire+ ndi kudalitsa+ m’dzina la Yehova. Iwo ndiwo ayenera kuthetsa mkangano uliwonse wokhudza choipa chilichonse chimene chachitika.+
5 “Ansembe, ana a Levi, azifika pafupi chifukwa ndi amene Yehova Mulungu wanu wawasankha kuti am’tumikire+ ndi kudalitsa+ m’dzina la Yehova. Iwo ndiwo ayenera kuthetsa mkangano uliwonse wokhudza choipa chilichonse chimene chachitika.+