Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 7:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Koma inu mudzawachitire zotsatirazi: Mudzagwetse maguwa awo ansembe+ ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzadule+ mizati yawo yopatulika+ ndi kutentha zifaniziro zawo zogoba.+

  • 1 Mafumu 14:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yehova adzawonongadi Isiraeli, ndipo zidzakhala ngati mmene bango limagwedezekera m’madzi,+ ndiponso adzazuladi+ Aisiraeli, kuwachotsa padziko labwinoli+ limene anapatsa makolo awo. Ndiyeno adzawabalalitsira+ kutsidya lina la Mtsinje,*+ popeza iwo anapanga mizati yawo yopatulika,+ n’kukwiyitsa+ nayo Yehova.

  • 1 Mafumu 16:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ahabu anaimikanso mzati wopatulika,+ ndipo iye anachita zinthu zambiri zokwiyitsa+ Yehova Mulungu wa Isiraeli kuposa mafumu onse a Isiraeli amene anakhalapo iye asanakhale.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena