Ekisodo 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Usaweramire milungu yawo kapena kuitumikira, ndipo usapange chilichonse chofanana ndi zifaniziro zawo,+ koma uzigwetse ndithu ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Deuteronomo 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mudzagwetse maguwa awo ansembe+ ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzatenthe mizati yawo yopatulika+ ndi kudula zifaniziro zogoba+ za milungu yawo, ndipo mudzafafanize mayina awo pamalo amenewo.+ Deuteronomo 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Ndipo usadziimikire chipilala chopatulika,+ chinthu chimene Yehova Mulungu wako amadana nacho kwambiri.+
24 Usaweramire milungu yawo kapena kuitumikira, ndipo usapange chilichonse chofanana ndi zifaniziro zawo,+ koma uzigwetse ndithu ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+
3 Mudzagwetse maguwa awo ansembe+ ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzatenthe mizati yawo yopatulika+ ndi kudula zifaniziro zogoba+ za milungu yawo, ndipo mudzafafanize mayina awo pamalo amenewo.+
22 “Ndipo usadziimikire chipilala chopatulika,+ chinthu chimene Yehova Mulungu wako amadana nacho kwambiri.+