Deuteronomo 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mudzagwetse maguwa awo ansembe+ ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzatenthe mizati yawo yopatulika+ ndi kudula zifaniziro zogoba+ za milungu yawo, ndipo mudzafafanize mayina awo pamalo amenewo.+
3 Mudzagwetse maguwa awo ansembe+ ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzatenthe mizati yawo yopatulika+ ndi kudula zifaniziro zogoba+ za milungu yawo, ndipo mudzafafanize mayina awo pamalo amenewo.+