1 Mafumu 16:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iye anali kuyenda m’njira zonse za Yerobowamu mwana wa Nebati,+ ndi m’tchimo lake limene anachimwitsa nalo Isiraeli mwa kukwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mafano awo opanda pake.+
26 Iye anali kuyenda m’njira zonse za Yerobowamu mwana wa Nebati,+ ndi m’tchimo lake limene anachimwitsa nalo Isiraeli mwa kukwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mafano awo opanda pake.+