1 Mafumu 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anawafafaniza chifukwa cha machimo onse a Basa ndi machimo amene Ela+ mwana wake anachita, ndiponso chifukwa cha machimo amene anachimwitsa nawo Aisiraeli. Iwo anakwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mafano awo opanda pake.+
13 Anawafafaniza chifukwa cha machimo onse a Basa ndi machimo amene Ela+ mwana wake anachita, ndiponso chifukwa cha machimo amene anachimwitsa nawo Aisiraeli. Iwo anakwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mafano awo opanda pake.+