2 Mafumu 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komabe, nawonso Ayudawo sanasunge malamulo a Yehova Mulungu+ wawo, koma anayenda motsatira malamulo amene Aisiraeli+ anapanga. Ezekieli 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Mng’ono wake Oholiba ataona zimenezi,+ anayamba kukonda chiwerewere chodziwononga nacho kuposa mkulu wake. Anayamba kuchita uhule kuposa dama la mkulu wake.+
19 Komabe, nawonso Ayudawo sanasunge malamulo a Yehova Mulungu+ wawo, koma anayenda motsatira malamulo amene Aisiraeli+ anapanga.
11 “Mng’ono wake Oholiba ataona zimenezi,+ anayamba kukonda chiwerewere chodziwononga nacho kuposa mkulu wake. Anayamba kuchita uhule kuposa dama la mkulu wake.+