9 Choncho ndinam’pereka m’manja mwa amuna amene anali kukhumba kugona naye.+ Ndinam’pereka m’manja mwa ana aamuna a ku Asuri amene iye anali kuwakhumba.+
2 Imbani mlandu mayi wanu.+ Muimbeni mlandu pakuti iye si mkazi wanga+ ndipo ine sindine mwamuna wake.+ Mayi wanuyo asiye dama lake ndi chigololo chake,*+