Yeremiya 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anayamba kuchita uhule chifukwa choona nkhani imeneyi mopepuka. Anali kuipitsa dzikolo+ ndi kuchita chigololo ndi miyala komanso mitengo.+ Ezekieli 16:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Unamanga malo ako okwerawo pamphambano iliyonse ya msewu+ ndipo unaipitsa kukongola kwako.+ Unayamba kukhanyulira munthu aliyense wodutsa+ n’kumachulukitsa zochita zako zauhule.+
9 Iye anayamba kuchita uhule chifukwa choona nkhani imeneyi mopepuka. Anali kuipitsa dzikolo+ ndi kuchita chigololo ndi miyala komanso mitengo.+
25 Unamanga malo ako okwerawo pamphambano iliyonse ya msewu+ ndipo unaipitsa kukongola kwako.+ Unayamba kukhanyulira munthu aliyense wodutsa+ n’kumachulukitsa zochita zako zauhule.+