Yesaya 57:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Gawo lako linali pamodzi ndi miyala yosalala ya m’chigwa.+ Iwo ndiwo anali gawo lako.+ Iwe unawathirira nsembe yachakumwa,+ ndiponso unawapatsa mphatso. Kodi ine ndingadzitonthoze ndi zinthu zimenezo?+ Yeremiya 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iwo akuuza mtengo kuti, ‘Ndinu bambo anga,’+ ndipo akuuza mwala kuti, ‘Ndinu amene munandibereka.’ Iwo andifulatira ndipo sanandisonyeze nkhope yawo.+ Koma tsoka likadzawagwera adzanena kuti, ‘Chonde, bwerani mudzatipulumutse!’+
6 “Gawo lako linali pamodzi ndi miyala yosalala ya m’chigwa.+ Iwo ndiwo anali gawo lako.+ Iwe unawathirira nsembe yachakumwa,+ ndiponso unawapatsa mphatso. Kodi ine ndingadzitonthoze ndi zinthu zimenezo?+
27 Iwo akuuza mtengo kuti, ‘Ndinu bambo anga,’+ ndipo akuuza mwala kuti, ‘Ndinu amene munandibereka.’ Iwo andifulatira ndipo sanandisonyeze nkhope yawo.+ Koma tsoka likadzawagwera adzanena kuti, ‘Chonde, bwerani mudzatipulumutse!’+