Ezekieli 23:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Adzakuchitira zimenezi chifukwa chakuti wachita uhule ndi mitundu ina ya anthu+ komanso chifukwa chakuti wadziipitsa ndi mafano awo onyansa.+
30 Adzakuchitira zimenezi chifukwa chakuti wachita uhule ndi mitundu ina ya anthu+ komanso chifukwa chakuti wadziipitsa ndi mafano awo onyansa.+