34 Yerusalemu, Yerusalemu! wakupha+ aneneri ndi kuponya miyala+ anthu otumidwa kwa iwe . . . mobwerezabwereza ndinafuna kusonkhanitsa ana ako monga mmene nkhuku yathadzi imasonkhanitsira anapiye ake m’mapiko ake,+ koma anthu inu simunafune zimenezo.+