Salimo 53:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi palibe aliyense wozindikira mwa anthu ochita zopweteka anzawowa,+Amene akudya anthu anga ngati chakudya?+Iwo sanaitane pa Yehova.+ Ezekieli 34:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu mukudya mafuta,+ ndipo mukuvala zovala zaubweya wa nkhosa. Mukupha+ nyama zonenepa,+ koma nkhosa simukuzidyetsa.
4 Kodi palibe aliyense wozindikira mwa anthu ochita zopweteka anzawowa,+Amene akudya anthu anga ngati chakudya?+Iwo sanaitane pa Yehova.+
3 Inu mukudya mafuta,+ ndipo mukuvala zovala zaubweya wa nkhosa. Mukupha+ nyama zonenepa,+ koma nkhosa simukuzidyetsa.