Salimo 53:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi palibe aliyense womvetsa zinthu pakati pa anthu ochita zoipawa? Iwo amadya anthu anga ngati kuti akudya chakudya. Ndipo sapemphera kwa Yehova.+
4 Kodi palibe aliyense womvetsa zinthu pakati pa anthu ochita zoipawa? Iwo amadya anthu anga ngati kuti akudya chakudya. Ndipo sapemphera kwa Yehova.+